Hello there my name is Japhet Malola stage name is EyooFourth am an upcoming artist based in Lilongwe I started music in 2018 because of one my family member who likes music and as i was attached to him slowly but surely i fell in love music.
Nyimbo yanga yoyamba kutulutsa anthu ambiri anayikonda pamene ena ankakaikira kunena kuti nyimboyo inali ndi unthenga wa ukulu womwe sizimangwirizana ndi sinkhu wanga, , nyimboyi Title yake inali #Ndi Ifebe prod by DjBrown
Izi zinandillimbikitsa kulowaso ku studio ndi kutulutsa nyimbo zina ngati #Iwe,OneDay,Nane& Inap 💥🙏🙌
Search my audios at www.olivia-music.com and www.oliviamusik.com
0 Comments
WELCOME VISITORS (LEAVE YOUR COMMENT)